Numeri 14:41 - Buku Lopatulika41 Ndipo Mose anati, Mutero chifukwa ninji kulakwira mau a Yehova, popeza simudzapindula nako? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201441 Ndipo Mose anati, Mutero chifukwa ninji kulakwira mau a Yehova, popeza simudzapindula nako? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa41 Koma Mose adati, “Chifukwa chiyani mukunyoza lamulo la Chauta, poti zimenezo sizidzatheka? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero41 Koma Mose anati, “Chifukwa chiyani simukumvera lamulo la Yehova? Zimenezi sizitheka! Onani mutuwo |