Numeri 14:40 - Buku Lopatulika40 Ndipo anauka mamawa, nakwera pamwamba paphiri, nati, Tili pano, tidzakwera kunka ku malo amene Yehova ananena; popeza tachimwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201440 Ndipo anauka mamawa, nakwera pamwamba pa phiri, nati, Tili pano, tidzakwera kunka ku malo amene Yehova ananena; popeza tachimwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa40 Adalaŵirira m'mamaŵa, ndipo adakwera cha ku dziko lamapiri, nati “Ife pano takonzeka kukwera mpaka kukafika ku malo amene Chauta adatilonjeza. Ndithu tachimwadi.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero40 Mmamawa tsiku linalo anapita mbali ya ku dziko la mapiri. Iwo anati, “Tachimwa, tipita ku dziko limene Yehova anatilonjeza.” Onani mutuwo |