Numeri 14:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo anati wina ndi mnzake, Tiike mtsogoleri, tibwerere ku Ejipito. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo anati wina ndi mnzake, Tiike mtsogoleri, tibwerere ku Ejipito. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Ndipo adayamba kuuzana kuti, “Tiyeni tisankhe mtsogoleri kuti tibwerere ku Ejipito.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Ndipo anawuzana wina ndi mnzake kuti, “Tiyeni tisankhe mtsogoleri ndipo tibwerere ku Igupto.” Onani mutuwo |