Numeri 14:38 - Buku Lopatulika38 Koma Yoswa mwana wa Nuni, ndi Kalebe mwana wa Yefune, anakhala ndi moyo mwa amuna aja adamukawo kukazonda dziko. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201438 Koma Yoswa mwana wa Nuni, ndi Kalebe mwana wa Yefune, anakhala ndi moyo mwa amuna aja adamukawo kukazonda dziko. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa38 Koma mwa anthu amene adapita kukazonda dziko aja, Yoswa mwana wa Nuni ndi Kalebe mwana wa Yefune ndiwo adatsala amoyo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero38 Mwa anthu amene anakaona dzikolo, Yoswa mwana wa Nuni ndi Kalebe mwana wa Yefune ndi okhawo amene anapulumuka. Onani mutuwo |