Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 14:36 - Buku Lopatulika

36 Ndipo amunawo, amene Mose anawatumiza kukazonda dziko, amene anabwera nadandaulitsa khamu lonse pa iye, poipsa mbiri ya dziko,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

36 Ndipo amunawo, amene Mose anawatumiza kukazonda dziko, amene anabwera nadandaulitsa khamu lonse pa iye, poipsa mbiri ya dziko,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

36 Anthu amene Mose adaŵatuma kuti akazonde dziko aja atabwerako, ena adayamba kuutsa mitima ya anthu kuti aukire Mose pakuŵauza zoipa za dzikolo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

36 Ndipo anthu amene Mose anawatuma kukazonda dziko aja anachoka pamaso pake nachititsa gulu lonse la anthu kuwukira Moseyo chifukwa chofalitsa mbiri yoyipa ya dzikolo.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 14:36
3 Mawu Ofanana  

Ndipo anthu anatsutsana ndi Mose, nanena, nati, Mwenzi titangomwalira muja abale athu anamwalira pamaso pa Yehova!


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa