Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 14:32 - Buku Lopatulika

32 Koma inu, mitembo yanu idzagwa m'chipululu muno.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

32 Koma inu, mitembo yanu idzagwa m'chipululu muno.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

32 Koma enanu, mitembo yanu idzakhala ili mbwee m'chipululu mommuno.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

32 Koma inu mitembo yanu idzakhala ngundangunda mʼchipululu muno.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 14:32
7 Mawu Ofanana  

Potero anawasamulira dzanja lake, kuti awagwetse m'chipululu:


mitembo yanu idzagwa m'chipululu muno; ndi owerengedwa anu onse, monga mwa kuwerenga kwani konse, kuyambira a zaka makumi awiri ndi mphambu, akudandaula pa Ine;


Koma pakati pao panalibe mmodzi wa iwo amene anawerengedwa ndi Mose ndi Aroni wansembe, amene anawerenga ana a Israele m'chipululu cha Sinai.


Popeza Yehova adanena za iwowa, Adzafatu m'chipululu. Ndipo sanatsalire mmodzi wa iwowa koma Kalebe mwana wa Yefune, ndi Yoswa mwana wa Nuni.


Ndipo Yehova anapsa mtima pa Israele, nawayendetsayendetsa m'chipululu zaka makumi anai, kufikira utatha mbadwo wonsewo udachita choipa pamaso pa Yehova.


Koma ochuluka a iwo Mulungu sanakondwere nao; pakuti anamwazika m'chipululu.


Koma anakwiya ndi ayani zaka makumi anai? Kodi si ndi awo adachimwawo, amene matupi ao adagwa m'chipululu?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa