Numeri 14:27 - Buku Lopatulika27 Ndileke khamu loipa ili lakudandaula pa Ine kufikira liti? Ndidamva madandaulo a ana a Israele, amene amandidandaulira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201427 Ndileke khamu loipa ili lakudandaula pa Ine kufikira liti? Ndidamva madandaulo a ana a Israele, amene amandidandaulira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa27 “Kodi anthu oipa chotereŵa, adzaleka liti kundiŵiringulira? Ndamva maŵiringulo ao amene akundichitira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero27 “Kodi anthu oyipawa adzangʼungʼudza ndi kutsutsana nane mpaka liti? Ndamva madandawulo a Aisraeli ongʼungʼudzawa. Onani mutuwo |