Numeri 14:26 - Buku Lopatulika26 Ndipo Yehova ananena kwa Mose ndi Aroni, nati, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Ndipo Yehova ananena kwa Mose ndi Aroni, nati, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Chauta adafunsa Mose ndi Aroni kuti, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Yehova anawuza Mose ndi Aaroni kuti, Onani mutuwo |