Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 14:25 - Buku Lopatulika

25 Koma Aamaleke ndi Akanani akhala m'chigwamo; tembenukani mawa, nimunke ulendo wanu kuchipululu, njira ya ku Nyanja Yofiira.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

25 Koma Aamaleke ndi Akanani akhala m'chigwamo; tembenukani mawa, nimumke ulendo wanu kuchipululu, njira ya ku Nyanja Yofiira.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

25 Tsono popeza kuti Aamaleke ndi Akanani amakhala m'zigwa, maŵa mubwerere, muyambepo ulendo wopita ku chipululu, mudzere ku Nyanja Yofiira.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

25 Ndipo popeza kuti Aamaleki ndi Akanaani akukhala ku chigwa, mawa mubwerere ndipo mupite ku chipululu podzera ku Nyanja Yofiira.”

Onani mutuwo Koperani




Numeri 14:25
7 Mawu Ofanana  

momwemo adzadya zipatso za mayendedwe ao, nadzakhuta zolingalira zao.


Aamaleke akhala m'dziko la kumwera; ndi Ahiti, ndi Ayebusi, ndi Aamori, akhala ku mapiri, ndi Akanani akhala kunyanja, ndi m'mphepete mwa Yordani.


Ndipo Yehova ananena kwa Mose ndi Aroni, nati,


Ndipo anati wina ndi mnzake, Tiike mtsogoleri, tibwerere ku Ejipito.


Koma inu, bwererani, mukani ulendo wanu kuchipululu, njira ya ku Nyanja Yofiira.


pakuti pakukwera iwo kuchokera ku Ejipito Israele anayenda m'chipululu mpaka Nyanja Yofiira, nafika ku Kadesi;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa