Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 14:16 - Buku Lopatulika

16 Popeza Yehova sanakhoze kuwalowetsa anthu awa m'dziko limene anawalumbirira, chifukwa chake anawapha m'chipululu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

16 Popeza Yehova sanakhoze kuwalowetsa anthu awa m'dziko limene anawalumbirira, chifukwa chake anawapha m'chipululu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

16 ‘Chauta waŵaphera m'chipululu anthuŵa, chifukwa choti sadathe kuŵaloŵetsa m'dziko limene adalumbira kuti adzaŵapatsa kuti likhale lao.’

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

16 ‘Yehova walephera kuwalowetsa anthuwo mʼdziko lomwe anawalonjeza molumbira, ndipo wawapha mʼchipululu.’

Onani mutuwo Koperani




Numeri 14:16
6 Mawu Ofanana  

Akaneneranji Aejipito, ndi kuti, Anawatulutsa ndi cholinga choipa, kuti awaphe m'mapiri, ndi kuwatha pankhope padziko lapansi? Pepani, lekani choipacho cha pa anthu anu.


Ndipo tsopano, ikuletu mphamvu ya Mbuye wanga, monga mudanena, ndi kuti,


kuti linganene dziko limene mudatitulutsako, Popeza Yehova sanakhoze kuwalowetsa m'dziko limene adanena nao, ndi popeza anadana nao, anawatulutsa kuti awaphe m'chipululu.


Ndipo Yoswa anati, Ha! Ambuye, Yehova, mwaolotseranji anthu awa pa Yordani, kutipereka ife m'dzanja la Aamori, kutiononga ife? Mwenzi titalola ndi kukhala tsidya lija la Yordani!


Akadzamva ichi Akanani ndi okhala m'dziko onse, adzatizinga ndi kuduliratu dzina lathu padziko lapansi; ndipo mudzachitiranji dzina lanu lalikulu?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa