Numeri 14:15 - Buku Lopatulika15 Ndipo mukapha anthu awa ngati munthu mmodzi, pamenepo amitundu amene adamva mbiri yanu adzanena, ndi kuti, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Ndipo mukapha anthu awa ngati munthu mmodzi, pamenepo amitundu amene adamva mbiri yanu adzanena, ndi kuti, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Tsopano mukaŵapha onse anthu ameneŵa, mitundu ina imene yamva mbiri yanu idzati, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Tsono mukawapha anthu onsewa nthawi imodzi, mayiko amene anamva za Inu adzati, Onani mutuwo |