Numeri 13:29 - Buku Lopatulika29 Aamaleke akhala m'dziko la kumwera; ndi Ahiti, ndi Ayebusi, ndi Aamori, akhala ku mapiri, ndi Akanani akhala kunyanja, ndi m'mphepete mwa Yordani. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201429 Aamaleke akhala m'dziko la kumwera; ndi Ahiti, ndi Ayebusi, ndi Aamori, akhala ku mapiri, ndi Akanani akhala kunyanja, ndi m'mphepete mwa Yordani. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa29 Aamaleke amakhala m'dziko lakumwera. Ahiti, Ayebusi ndi Aamori amakhala m'dziko lamapiri. Akanani amakhala m'mphepete mwa nyanja ndi m'mphepete mwa mtsinje wa Yordani.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero29 Aamaleki amakhala ku Negevi, Ahiti, Ayebusi ndi Aamori amakhala mʼdziko la mapiri ndipo Akanaani amakhala pafupi ndi nyanja, mʼmbali mwa Yorodani.” Onani mutuwo |