Numeri 13:25 - Buku Lopatulika25 Pamenepo anabwerera atazonda dziko, atatha masiku makumi anai. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Pamenepo anabwerera atazonda dziko, atatha masiku makumi anai. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Patapita masiku makumi anai, anthu aja adabwerako kumene adakazonda dziko kuja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Patapita masiku makumi anayi, anthu aja anabwerako kokazonda dziko lija. Onani mutuwo |