Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 13:24 - Buku Lopatulika

24 Malowa anawatcha chigwa cha Esikolo, chifukwa cha tsangolo ana a Israele analichekako.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

24 Malowa anawatcha chigwa cha Esikolo, chifukwa cha tsangolo ana a Israele analichekako.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

24 Malowo adaŵatcha chigwa cha Esikolo, chifukwa cha tsango lamphesa limene anthu aja adathyola kumeneko.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

24 Malo amenewo anawatcha chigwa cha Esikolo chifukwa cha phava la mphesa limene Aisraeli anadula kumeneko.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 13:24
3 Mawu Ofanana  

Ndipo anadza ku chigwa cha Esikolo, nachekako tsango limodzi la mphesa, nalisenza awiri mopika; anabwera nazonso makangaza ndi nkhuyu.


Pamenepo anabwerera atazonda dziko, atatha masiku makumi anai.


Popeza atakwera kunka ku chigwa cha Esikolo, naona dziko, anafoketsa mtima wa ana a Israele, kuti asalowe dzikoli Yehova adawapatsa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa