Numeri 13:26 - Buku Lopatulika26 Ndipo anamuka, nadza kwa Mose, ndi Aroni, ndi khamu lonse la ana a Israele, ku chipululu cha Parani ku Kadesi; ndipo anabwezera mau iwowa, ndi khamu lonse, nawaonetsa zipatso za dzikoli. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Ndipo anamuka, nadza kwa Mose, ndi Aroni, ndi khamu lonse la ana a Israele, ku chipululu cha Parani ku Kadesi; ndipo anabwezera mau iwowa, ndi khamu lonse, nawaonetsa zipatso za dzikoli. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Adabwera kwa Mose ndi Aroni ndi kwa mpingo wa Aisraele m'chipululu cha Parani ku Kadesi. Adasimbira Mose ndi Aroni ndi mpingo wonse za ulendo wao naŵaonetsa zipatso za ku dzikolo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Ndipo atabwerako anapita kwa Mose ndi Aaroni ndi kwa Aisraeli onse ku Kadesi mʼchipululu cha Parani. Kumeneko anafotokozera anthu onse nawaonetsanso zipatso za mʼdzikolo. Onani mutuwo |