Numeri 13:18 - Buku Lopatulika18 mukaone dziko umo liliri; ndi anthu akukhala m'mwemo, ngati ali amphamvu kapena ofooka, ngati achepa kapena achuluka; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 mukaone dziko umo liliri; ndi anthu akukhala m'mwemo, ngati ali amphamvu kapena ofooka, ngati achepa kapena achuluka; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Mukaone dzikolo kuti ndi lotani, ndipo ngati anthu am'dzikomo ngamphamvu kapena opanda mphamvu, ngati ngoŵerengeka kapena ambiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Mukaone dzikolo kuti ndi lotani ndi anthu okhala mʼmenemo ngati ndi amphamvu kapena ofowoka, ochepa kapena ambiri. Onani mutuwo |