Numeri 13:19 - Buku Lopatulika19 ndi umo liliri dzikoli lokhalamo iwo, ngati lokoma, kapena loipa; ndi umo iliri mizindayo akhalamo iwo, ngati akhala poyera kapena m'malinga; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 ndi umo liliri dzikoli lokhalamo iwo, ngati lokoma, kapena loipa; ndi umo iliri midziyo akhalamo iwo, ngati akhala poyera kapena m'malinga; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Mukaone ngati dziko limene akukhalamolo ndi labwino kapena loipa, ngati mizinda imene amakhalamo ndi yamahema kapena yamalinga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Nanga dziko limene akukhalako ndi lotani? Ndi labwino kapena loyipa? Mizinda imene akukhalamo ndi yotani? Kodi ilibe malinga kapena ndi ya malinga? Onani mutuwo |