Numeri 12:3 - Buku Lopatulika3 Koma munthuyu Mose ndiye wofatsa woposa anthu onse a padziko lapansi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Koma munthuyu Mose ndiye wofatsa woposa anthu onse a pa dziko lapansi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Koma Mose anali munthu wofatsa kupambana anthu onse a pa dziko lapansi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 (Koma Mose anali munthu wodzichepetsa kwambiri kuposa munthu aliyense pa dziko lapansi). Onani mutuwo |