Numeri 11:14 - Buku Lopatulika14 Sinditha kuwasenza anthu awa onse ndekha, pakuti andilemera ine. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Sinditha kuwasenza anthu awa onse ndekha, pakuti andilemera ine. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Ine sindingathe kuŵasamala ndekha anthu onseŵa. Katundu ameneyu sindingathe kumsenza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Sindingathe kusamala anthu onsewa ndekha. Katundu ameneyu ndi wolemera kwambiri kwa ine. Onani mutuwo |