Numeri 11:13 - Buku Lopatulika13 Ndidzaiona kuti nyama yakuwapatsa anthu awa onse? Pakuti amalirira ine, ndi kuti, Tipatseni nyama, tidye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndidzaiona kuti nyama yakuwapatsa anthu awa onse? Pakuti amalirira ine, ndi kuti, Tipatseni nyama, tidye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Kodi nyama yoti ndiŵapatse anthu onseŵa, ndiitenga kuti? Iwowo akundilirira ine kuti, ‘Tipatseni nyama, tidye.’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Ndingayipeze kuti nyama yoti anthu onsewa adye? Iwowa akulirira ine kuti, ‘Tipatse nyama tidye!’ Onani mutuwo |