Numeri 11:15 - Buku Lopatulika15 Ndipo ngati mundichitira chotero, mundiphetu tsopano apa, ngati ndapeza ufulu pamaso panu, ndisayang'ane tsoka langa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Ndipo ngati mundichitira chotero, mundiphetu tsopano apa, ngati ndapeza ufulu pamaso panu, ndisayang'ane tsoka langa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Ndipotu mukafuna kundichita zimenezi, mungondipha basi, ngati mwandikomera mtima, kuti ndisaonenso mavutowo.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Ngati umu ndi mmene muzichitira nane, chonde ingondiphani pompano. Koma ngati mwandikomera mtima ndiye ndisaonenso mavutowa.” Onani mutuwo |