Numeri 10:29 - Buku Lopatulika29 Ndipo Mose anati kwa Hobabu mwana wa Reuwele Mmidiyani mpongozi wa Mose, Ife tili kuyenda kunka ku malo amene Yehova anati, Ndidzakupatsani awa; umuke nafe, tidzakuchitira zokoma; popeza Yehova wanenera Israele zokoma. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201429 Ndipo Mose anati kwa Hobabu mwana wa Reuwele Mmidiyani mpongozi wa Mose, Ife tili kuyenda kunka ku malo amene Yehova anati, Ndidzakupatsani awa; umuke nafe, tidzakuchitira zokoma; popeza Yehova wanenera Israele zokoma. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa29 Mose adauza Hobaba, mwana wa Reuele Mmidiyani, mpongozi wake uja, kuti, “Tikupita ku malo amene Chauta adati, ‘Ndidzakupatsani.’ Tiyeni tipite limodzi, ndipo tidzakuchitirani zabwino, pakuti Chauta walonjeza Aisraele zinthu zabwino.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero29 Ndipo Mose anawuza Hobabu mwana wa Reueli Mmidiyani, mpongozi wa Mose kuti, “Tikunyamuka kupita ku malo amene Yehova anati, ‘Ndidzakupatsani.’ Tiye upite nafe ndipo tidzakusamalira bwino, pakuti Yehova analonjeza zinthu zabwino kwa Israeli.” Onani mutuwo |