Numeri 10:28 - Buku Lopatulika28 Potero maulendo a ana a Israele anakhala monga mwa magulu ao; nayenda ulendo wao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201428 Potero maulendo a ana a Israele anakhala monga mwa magulu ao; nayenda ulendo wao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa28 Umenewu ndiwo mndandanda wa kayendedwe ka Aisraele, pamene ankanyamuka ulendo wao m'magulumagulu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero28 Umenewu ndiwo unali mndandanda wa kayendedwe ka magulu a Aisraeli pamene ankanyamuka ulendo wawo mʼmagulumagulu. Onani mutuwo |