Numeri 10:27 - Buku Lopatulika27 Ndi pa gulu la fuko la ana a Nafutali anayang'anira Ahira mwana wa Enani. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201427 Ndi pa gulu la fuko la ana a Nafutali anayang'anira Ahira mwana wa Enani. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa27 Mtsogoleri wa gulu la fuko la Nafutali anali Ahira mwana wa Enani. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero27 ndipo mtsogoleri wa mtundu wa Nafutali anali Ahira mwana wa Enani. Onani mutuwo |