Numeri 10:26 - Buku Lopatulika26 Ndi pa gulu la fuko la ana a Asere anayang'anira Pagiyele mwana wa Okarani. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Ndi pa gulu la fuko la ana a Asere anayang'anira Pagiyele mwana wa Okarani. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Mtsogoleri wa gulu la fuko la Asere anali Pagiyele mwana wa Okarani. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Pagieli mwana wa Okirani ndiye anali mtsogoleri wa fuko la Aseri, Onani mutuwo |