Numeri 1:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo maina a amuna amene aime nanu ndi awa: wa Rubeni, Elizuri mwana wa Sedeuri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo maina a amuna amene aime nanu ndi awa: wa Rubeni, Elizuri mwana wa Sedeuri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Maina a anthu okuthandizaniwo ndi aŵa: fuko la Rubeni, akuthandizeni ndi Elizuri mwana wa Sedeuri; Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Mayina a anthu amene akuthandizeniwo ndi awa: Elizuri mwana wa Sedeuri, kuchokera ku fuko la Rubeni, Onani mutuwo |