Numeri 1:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo pamodzi ndi inu pakhale munthu mmodzi wa mafuko onse; yense mkulu wa nyumba ya kholo lake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo pamodzi ndi inu pakhale munthu mmodzi wa mafuko onse; yense mkulu wa nyumba ya kholo lake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Pa fuko lililonse mutenge munthu mmodzi, mtsogoleri wa banja lake, kuti akuthandizeni pa ntchito yanuyo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Munthu mmodzi wochokera ku fuko lililonse yemwe ndi mtsogoleri wa banja lake, ndiye akuthandizeni pa ntchitoyi. Onani mutuwo |