Numeri 1:46 - Buku Lopatulika46 inde owerengedwa onse ndiwo zikwi mazana asanu ndi limodzi mphambu zitatu kudza mazana asanu ndi makumi asanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201446 inde owerengedwa onse ndiwo zikwi mazana asanu ndi limodzi mphambu zitatu kudza mazana asanu ndi makumi asanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa46 adapezeka kuti ali 603,550. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero46 Chiwerengero cha anthu onse pamodzi chinali 603,550. Onani mutuwo |