Numeri 1:45 - Buku Lopatulika45 Potero owerengedwa onse a ana a Israele monga mwa nyumba za makolo ao, kuyambira a zaka makumi awiri ndi mphambu, onse akutulukira kunkhondo mu Israele; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201445 Potero owerengedwa onse a ana a Israele monga mwa nyumba za makolo ao, kuyambira a zaka makumi awiri ndi mphambu, onse akutulukira kunkhondo m'Israele; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa45 Choncho amuna onse a mu Israele otha kumenya nkhondo, a zaka 20 ndi a zaka zopitirirapo, potsata banja la makolo ao, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero45 Aisraeli onse a zaka makumi awiri kapena kupitirirapo, omwe akanatha kugwira ntchito ya usilikali mʼgulu lankhondo la Israeli anawawerenga monga mwa mabanja awo. Onani mutuwo |