Numeri 1:44 - Buku Lopatulika44 Iwo ndiwo amene anawerengedwa, amene Mose anawerenga pamodzi ndi Aroni, ndi akalonga a Israele, ndiwo amuna khumi ndi awiri; yense kunenera nyumba ya kholo lake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201444 Iwo ndiwo amene anawerengedwa, amene Mose anawerenga pamodzi ndi Aroni, ndi akalonga a Israele, ndiwo amuna khumi ndi awiri; yense kunenera nyumba ya kholo lake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa44 Ameneŵa ndiwo anthu amene Mose ndi Aroni adaŵaŵerenga, mothandizidwa ndi atsogoleri a Aisraele khumi ndi aŵiri amene ankaimirira mafuko ao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero44 Amenewa ndiwo anthu amene Mose ndi Aaroni anawawerenga mothandizidwa ndi atsogoleri khumi ndi awiri a Israeli, aliyense kuyimira fuko lake. Onani mutuwo |