Numeri 1:43 - Buku Lopatulika43 owerengedwa ao a fuko la Nafutali, ndiwo zikwi makumi asanu mphambu zitatu kudza mazana anai. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201443 owerengedwa ao a fuko la Nafutali, ndiwo zikwi makumi asanu mphambu zitatu kudza mazana anai. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa43 Tsono ataŵerenga maina onse a m'fuko la Nafutali, adapezeka kuti ali 53,400. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero43 Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Nafutali chinali 53,400. Onani mutuwo |