Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 1:43 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

43 Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Nafutali chinali 53,400.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

43 owerengedwa ao a fuko la Nafutali, ndiwo zikwi makumi asanu mphambu zitatu kudza mazana anai.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

43 owerengedwa ao a fuko la Nafutali, ndiwo zikwi makumi asanu mphambu zitatu kudza mazana anai.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

43 Tsono ataŵerenga maina onse a m'fuko la Nafutali, adapezeka kuti ali 53,400.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 1:43
4 Mawu Ofanana  

Kuchokera mwa zidzukulu za Nafutali: Aamuna onse a zaka makumi awiri kapena kupitirirapo, omwe akanatha kugwira ntchito ya usilikali anawalemba mayina awo monga mwa mbiri ya mafuko awo ndi mabanja awo.


Amenewa ndiwo anthu amene Mose ndi Aaroni anawawerenga mothandizidwa ndi atsogoleri khumi ndi awiri a Israeli, aliyense kuyimira fuko lake.


Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 53,400.


Awa ndiwo anali mafuko a Nafutali. Onse amene anawerengedwa analipo 45,400.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa