Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Nehemiya 9:9 - Buku Lopatulika

9 Ndipo munapenya msauko wa makolo athu mu Ejipito, nimunamva kufuula kwao ku Nyanja Yofiira,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Ndipo munapenya msauko wa makolo athu m'Ejipito, nimunamva kufuula kwao ku Nyanja Yofiira,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 “Mudaona kuzunzika kwa makolo athu ku Ejipito kuja, ndipo mudamva kulira kwao ku Nyanja Yofiira.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 “Munaona kuzunzika kwa makolo athu ku Igupto. Munamva kufuwula kwawo pa Nyanja Yofiira.

Onani mutuwo Koperani




Nehemiya 9:9
8 Mawu Ofanana  

Ndipo Israele anaiona ntchito yaikulu imene Yehova anachitira Aejipito, ndipo anthuwo anaopa Yehova; nakhulupirira Yehova ndi mtumiki wake Mose.


Ndipo Mulungu anapenya Aisraele, ndi Mulungu anadziwa.


Muka, nukasonkhanitse akulu a Israele, nunene nao, Yehova, Mulungu wa makolo anu anandionekera ine, Mulungu wa Abrahamu, Isaki ndi Yakobo, ndi kuti, Ndakuzondani ndithu, ndi kuona chomwe akuchitirani mu Ejipito;


tsiku lomwelo ndinawakwezera dzanja langa kuwatulutsa m'dziko la Ejipito, kunka nao kudziko ndinawazondera, moyenda mkaka ndi uchi, ndilo lokometsetsa mwa maiko onse;


Kuona ndaona choipidwa nacho anthu anga ali mu Ejipito, ndipo amva kubuula kwao; ndipo ndatsika kuwalanditsa; ndipo tsopano, tiye kuno, ndikutume ku Ejipito.


Ndipo mtundu umene udzawayesa akapolo, ndidzauweruza Ine, anatero Mulungu; ndipo zitapita izi adzatuluka, nadzanditumikira Ine m'malo muno.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa