Nehemiya 9:2 - Buku Lopatulika2 Nadzipatula a mbumba ya Israele kwa alendo onse, naimirira, nawulula zochimwa zao, ndi mphulupulu za makolo ao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Nadzipatula a mbumba ya Israele kwa alendo onse, naimirira, nawulula zochimwa zao, ndi mphulupulu za makolo ao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Aisraele atadzipatula pakati pa anthu a mitundu ina, adaimirira, nayamba kuulula machimo ao ndi zolakwa za makolo ao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Aisraeliwa anadzipatula pakati pa anthu a mitundu ina ndipo anayimirira nayamba kuwulula machimo awo ndi zolakwa za makolo awo. Onani mutuwo |