Nehemiya 9:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo tsiku la makumi awiri mphambu anai la mwezi uno ana a Israele anasonkhana ndi kusala, ndi kuvala chiguduli, ndipo anali ndi fumbi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo tsiku la makumi awiri mphambu anai la mwezi uno ana a Israele anasonkhana ndi kusala, ndi kuvala chiguduli, ndipo anali ndi fumbi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Tsono tsiku la 24 la mwezi womwewo, Aisraele onse adasonkhana kuti asale chakudya, kuvala chiguduli ndi kudzithira dothi pa mutu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Pa tsiku la 24 la mwezi womwewo, Aisraeli anasonkhana pamodzi ndi kusala chakudya, kuvala ziguduli ndi kudzithira dothi pa mutu. Onani mutuwo |