Nehemiya 7:71 - Buku Lopatulika71 Enanso a akulu a nyumba za makolo anapereka kuchuma cha ntchitoyi, madariki agolide zikwi makumi awiri, ndi miyeso ya siliva zikwi ziwiri mphambu mazana awiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201471 Enanso a akulu a nyumba za makolo anapereka kuchuma cha ntchitoyi, madariki agolide zikwi makumi awiri, ndi miyeso ya mina ya siliva zikwi ziwiri mphambu mazana awiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa71 Atsogoleri ena a mabanja adapereka mosungira chumamo ndalama zagolide za makilogaramu 168, ndiponso ndalama zasiliva za makilogaramu 1,250. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero71 Atsogoleri ena amabanja anapereka ku thumba losungira chuma ndalama zagolide zokwana makilogalamu 168, ndiponso ndalama za siliva zokwana makilogalamu 1,250. Onani mutuwo |