Nehemiya 7:66 - Buku Lopatulika66 Msonkhano wonse pamodzi ndiwo zikwi makumi anai ndi ziwiri mphambu mazana atatu kudza makumi asanu ndi limodzi, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201466 Msonkhano wonse pamodzi ndiwo zikwi makumi anai ndi ziwiri mphambu mazana atatu kudza makumi asanu ndi limodzi, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa66 Chiŵerengero cha anthu onse obwerako ku ukapolo aja chinali 42,360. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero66 Chiwerengero chonse cha anthuwa chinali 42,360. Onani mutuwo |