Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Nehemiya 7:40 - Buku Lopatulika

40 Ana a Imeri, chikwi chimodzi mphambu makumi asanu kudza awiri.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

40 Ana a Imeri, chikwi chimodzi mphambu makumi asanu kudza awiri.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

40 A banja la Imara 1,052.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

40 Zidzukulu za Imeri 1,052

Onani mutuwo Koperani




Nehemiya 7:40
5 Mawu Ofanana  

wakhumi ndi chisanu Biliga, wakhumi ndi chisanu ndi chimodzi Imeri,


Ana a Imeri, chikwi chimodzi mphambu makumi asanu kudza awiri.


Potsatizana nao anakonza Zadoki mwana wa Imeri pandunji pa nyumba yake. Ndi potsatizana naye anakonza Semaya mwana wa Sekaniya, wosunga Chipata cha Kum'mawa.


Ansembe: ana a Yedaya, a nyumba ya Yesuwa, mazana asanu ndi anai mphambu makumi asanu ndi awiri kudza atatu.


Ana a Pasuri, chikwi chimodzi mphambu mazana awiri kudza makumi anai ndi asanu ndi awiri.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa