Nehemiya 7:39 - Buku Lopatulika39 Ansembe: ana a Yedaya, a nyumba ya Yesuwa, mazana asanu ndi anai mphambu makumi asanu ndi awiri kudza atatu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201439 Ansembe: ana a Yedaya, a nyumba ya Yesuwa, mazana asanu ndi anai mphambu makumi asanu ndi awiri kudza atatu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa39 Ansembe anali aŵa: a banja la Yedaya, ndiye kuti zidzukulu za Yesuwa, 973. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero39 Ansembe anali awa: A banja la Yedaya (ndiye kuti zidzukulu za Yesuwa) 973 Onani mutuwo |