Nehemiya 7:38 - Buku Lopatulika38 Ana a Senaa, zikwi zitatu mphambu mazana asanu ndi anai kudza makumi atatu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201438 Ana a Senaa, zikwi zitatu mphambu mazana asanu ndi anai kudza makumi atatu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa38 A ku Senaya 3,930. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero38 Zidzukulu za Senaya 3,930. Onani mutuwo |