Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Nehemiya 7:37 - Buku Lopatulika

37 Ana a Lodi, Hadidi, ndi Ono, mazana asanu ndi awiri mphambu makumi awiri kudza mmodzi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

37 Ana a Lodi, Hadidi, ndi Ono, mazana asanu ndi awiri mphambu makumi awiri kudza mmodzi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

37 A ku Lodi, Hadidi ndi Ono 721.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

37 Zidzukulu za Lodi, Hadidi ndi Ono 721

Onani mutuwo Koperani




Nehemiya 7:37
8 Mawu Ofanana  

Ndi ana a Elipaala: Eberi, ndi Misamu, ndi Semedi, amene anamanga Ono, ndi Lodi ndi midzi yake,


Ana a Lodi, Hadidi, ndi Ono, mazana asanu ndi awiri mphambu makumi awiri kudza asanu.


anatumiza mau kwa ine Sanibalati ndi Gesemu, kuti, Tiyeni tikomane kumidzi ya ku Chigwa cha Ono; koma analingirira za kundichitira choipa.


Ana a Yeriko, mazana atatu mphambu makumi anai kudza asanu.


Ana a Senaa, zikwi zitatu mphambu mazana asanu ndi anai kudza makumi atatu.


Koma kunali, pakupita Petro ponseponse, anatsikiranso kwa oyera mtima akukhala ku Lida.


Ndipo anamuona iye onse akukhala ku Lida ndi ku Saroni, natembenukira kwa Ambuye amenewa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa