Nehemiya 6:8 - Buku Lopatulika8 Koma ndinamtumizira mau, akuti, Palibe zinthu zotere zonga unenazi, koma uzilingirira mumtima mwako. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Koma ndinamtumizira mau, akuti, Palibe zinthu zotere zonga unenazi, koma uzilingirira mumtima mwako. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Apo ndidamtumizira mau akuti, “Pa zimene mukunenazi, palibe chimene chidachitikapo. Zonsezi mukungoziganiza nokha.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Ine ndinatumiza yankho ili: “Pa zimene mukunenazo, palibe chimene chinachitikapo. Inu mukungozipeka mʼmutu mwanu.” Onani mutuwo |