Nehemiya 6:5 - Buku Lopatulika5 Pamenepo Sanibalati anatuma mnyamata wake kwa ine kachisanu, ndi kalata yosatseka m'dzanja mwake; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Pamenepo Sanibalati anatuma mnyamata wake kwa ine kachisanu, ndi kalata wosatseka m'dzanja mwake; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Pamenepo Sanibalati adatumanso wantchito wake kachisanu kwa ine. Iye anali ndi kalata yosamata m'manja mwake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Tsono kachisanu, Sanibalati anatumiza wantchito wake ndi kalata yosamata. Onani mutuwo |