Nehemiya 6:4 - Buku Lopatulika4 Nanditumizira ine mau otere kanai; ndinawabwezeranso mau momwemo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Nanditumizira ine mau otere kanai; ndinawabwezeranso mau momwemo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Tsono adanditumizira mau okhaokhawo kanai konse, ndipo ndidaŵayankha chimodzimodzi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Ananditumizira uthenga umodzimodzi omwewu kanayi ndipo ndinawayankha chimodzimodzi. Onani mutuwo |