Nehemiya 6:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo ndinawatumizira mithenga, ndi kuti, Ndilikuchita ntchito yaikulu, sindingathe kutsika; ndiidulirenji padera ntchito poileka ine, ndi kukutsikirani? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo ndinawatumizira mithenga, ndi kuti, Ndilikuchita ntchito yaikulu, sindikhoza kutsika; ndiidulirenji padera ntchito poileka ine, ndi kukutsikirani? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Nchifukwa chake ndidaŵatumira amithenga kukaŵauza kuti, “Ine kuno ndili pa ntchito yaikulu, sindingathe kuchoka kuti ndibwere kumeneko. Kodi ntchito iime, pofuna kuti ndibwere kumeneko?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Choncho ine ndinatuma amithenga ndi yankho ili: “Ine ndikugwira ntchito yayikulu kuno ndipo sindingathe kubwera kumeneko. Kodi ntchito iyime pofuna kuti ndibwere kumeneko?” Onani mutuwo |