Nehemiya 6:2 - Buku Lopatulika2 anatumiza mau kwa ine Sanibalati ndi Gesemu, kuti, Tiyeni tikomane kumidzi ya ku Chigwa cha Ono; koma analingirira za kundichitira choipa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 anatumiza mau kwa ine Sanibalati ndi Gesemu, kuti, Tiyeni tikomane kumidzi ya ku Chigwa cha Ono; koma analingirira za kundichitira choipa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Tsono Sanibalati ndi Gesemu adanditumizira mau onena kuti, “Mubwere, tidzakumane pa mudzi wina m'chigwa cha Ono.” Ankafuna kukandichita chiwembu kumeneko. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Sanibalati ndi Gesemu, ananditumizira uthenga uwu: “Bwerani tidzakumane pa mudzi wina ku chigwa cha Ono.” Koma iwo anakonzekera kuti akandichite chiwembu kumeneko. Onani mutuwo |