Nehemiya 5:3 - Buku Lopatulika3 Panali enanso akuti, Tili kupereka chikole minda yathu, ndi minda yathu yampesa ndi nyumba zathu; kuti tilandire tirigu chifukwa cha njalayi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Panali enanso akuti, Tili kupereka chikole minda yathu, ndi minda yathu yampesa ndi nyumba zathu; kuti tilandire tirigu chifukwa cha njalayi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Panalinso ena amene ankati, “Ife tikuchita kupereka minda yathu, mitengo yathu yamphesa, pamodzi ndi nyumba zathu, ngati chikole, kuti tipeze tirigu, poti njala yatipha.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Panali ena amene ankanena kuti, “Ife tikuchita kupereka minda yathu, mitengo yathu ya mphesa ndi nyumba zathu ngati chikole kuti tipeze tirigu chifukwa njala yakula.” Onani mutuwo |