Nehemiya 5:16 - Buku Lopatulika16 Ndiponso ndinalimbikira ntchito ya linga ili, ngakhale dziko sitinaligule, ndi anyamata anga onse anasonkhanira ntchito komweko. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ndiponso ndinalimbikira ntchito ya linga ili, ngakhale dziko sitinaligula, ndi anyamata anga onse anasonkhanira ntchito komweko. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Ndiponso ndinkakangamira pa ntchito yomanga makoma a mzinda, osafuna kupata minda. Antchito anga onsenso anali komweko, ndidaaŵalamula kuti adzipereke pa ntchito yokhayokhayo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Ndiponso ndinadzipereka kugwira ntchito yomanga khoma la mzinda wa Yerusalemu popanda ngakhale kugulapo munda. Antchito anganso anasonkhana komweko kuti agwire ntchito ndipo sitinafunenso malo ena. Onani mutuwo |