Nehemiya 4:19 - Buku Lopatulika19 Ndipo ndinati kwa aufulu, ndi olamulira, ndi anthu otsala, Ntchito ndiyo yochuluka ndi yachitando, ndi ife tili palakepalake palingapo, yense atalikizana ndi mnzake; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Ndipo ndinati kwa aufulu, ndi olamulira, ndi anthu otsala, Ntchito ndiyo yochuluka ndi yachitando, ndi ife tili palakepalake palingapo, yense atalikizana ndi mnzake; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Ndidaŵauza atsogoleri ndi akuluakulu ndiponso anthu ena onse aja kuti, “Ntchitoyi njaikulu, ili pa dera lalikulu, ndipo ifeyo takhala motayanatayana kwambiri pa khoma. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Ndipo ine ndinati kwa anthu olemekezeka ndi anthu ena onse, “Ntchitoyi ndi yayikulu ndipo ili padera lalikulu ndipo ifeyo takhala motayanatayana kwambiri pa khoma. Onani mutuwo |