Nehemiya 4:20 - Buku Lopatulika20 paliponse mukumva mau a lipenga, musonkhanire komweko kwa ife; Mulungu wathu adzatigwirira nkhondo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 paliponse mukumva mau a lipenga, musonkhanire komweko kwa ife; Mulungu wathu adzatigwirira nkhondo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Tsono kumene muliriko mukamva kulira kwa lipenga, mudzasonkhane msanga kumene tili ife kuno. Mulungu wathu adzatimenyera nkhondo.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Tsono kulikonse kumene muliko, mukamva kulira kwa lipenga bwerani mudzasonkhane kumene kuli ine kuno. Mulungu wathu adzatimenyera nkhondo.” Onani mutuwo |